baibo ya achichepele liliko pofuna kuti yesu kristu aziwike ku ana kupitila mu nkhani za baibo zoonesera ndi zithu zosiyana napa midiya, kuongezelapo World wide web, ma celula foni/PDA\’s pepala yosindikiziwa mumitundu ndi kuika mitundu kuma buku, muchilankhulo chonse chimene mwana anga kambe.
nkhani za baibo zimenezi zifunika kugawila achichepele okwanila ngati 1.8 biliyoni pa ziko lonse mwaulele ngati nikotheka.